Yohane 16:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chimodzimodzi inunso, panopa muli ndi chisoni. Koma ndidzakuonaninso ndipo mitima yanu idzasangalala.+ Palibenso amene adzachititse kuti musiye kusangalala.
22 Chimodzimodzi inunso, panopa muli ndi chisoni. Koma ndidzakuonaninso ndipo mitima yanu idzasangalala.+ Palibenso amene adzachititse kuti musiye kusangalala.