Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 4:16, 17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 anthu amene ankakhala mumdima anaona kuwala kwakukulu, ndipo anthu amene ankakhala mʼdera lamthunzi wa imfa, kuwala+ kunawaunikira.”+ 17 Kuyambira nthawi imeneyo, Yesu anayamba kulalikira kuti: “Lapani, chifukwa Ufumu wakumwamba wayandikira.”+

  • Yohane 3:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Kuwala kwafika mʼdziko+ koma mʼmalo mokonda kuwala anthu akukonda mdima popeza ntchito zawo nʼzoipa, nʼchifukwa chake adzaweruzidwe.

  • Yohane 12:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Ndabwera monga kuwala mʼdziko,+ kuti aliyense wokhulupirira ine asapitirize kukhala mumdima.+

  • 1 Yohane 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Komabe, ndikukulemberani lamulo latsopano limene Yesu ankalitsatira, limenenso inuyo mukulitsatira, chifukwa mdima ukupita ndipo kuwala kwenikweni kwayamba kale kuunika.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena