Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 53:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma Yehova ndi amene anafuna* kuti mtumiki wake aphwanyidwe ndipo anamulola kuti adwale.

      Ngati mungapereke moyo wake kuti ukhale nsembe yakupalamula,+

      Iye adzaona ana ake,* adzakhala ndi moyo kwa nthawi yaitali,+

      Ndipo kudzera mwa iye, zofuna za* Yehova zidzatheka.+

  • Luka 24:44
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 Ndiyeno anawauza kuti: “Pamene ndinali nanu limodzi ndinakuuzani mawu akuti,+ zonse zokhudza ine zimene zinalembedwa mʼChilamulo cha Mose, zimene aneneri analemba komanso zimene zinalembedwa mʼMasalimo ziyenera kukwaniritsidwa.”+

  • Machitidwe 2:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Munthu ameneyu, amene anaperekedwa mwa kufuna kwa Mulungu+ ndi kudziwiratu kwake zamʼtsogolo, munachititsa kuti aphedwe pokhomeredwa pamtengo ndi anthu osamvera malamulo.+

  • 1 Petulo 1:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Zoonadi, Mulungu anasankhiratu Khristu anthu asanayambe kuberekana padziko lapansi,+ koma anaonekera pa nthawi yamapeto chifukwa cha inuyo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena