Zekariya 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako ndinawauza kuti: “Ngati mukuona kuti nʼzoyenera, ndipatseni malipiro anga. Koma ngati mukuona kuti nʼzosayenera musandipatse.” Iwo anandilipira* ndalama 30 zasiliva.+ Mateyu 26:14, 15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako mmodzi wa ophunzira 12 aja, amene ankadziwika kuti Yudasi Isikariyoti,+ anapita kwa ansembe aakulu+ 15 nʼkuwafunsa kuti: “Kodi mudzandipatsa chiyani ndikamupereka kwa inu?”+ Iwo anamulonjeza ndalama 30 zasiliva.+
12 Kenako ndinawauza kuti: “Ngati mukuona kuti nʼzoyenera, ndipatseni malipiro anga. Koma ngati mukuona kuti nʼzosayenera musandipatse.” Iwo anandilipira* ndalama 30 zasiliva.+
14 Kenako mmodzi wa ophunzira 12 aja, amene ankadziwika kuti Yudasi Isikariyoti,+ anapita kwa ansembe aakulu+ 15 nʼkuwafunsa kuti: “Kodi mudzandipatsa chiyani ndikamupereka kwa inu?”+ Iwo anamulonjeza ndalama 30 zasiliva.+