Genesis 35:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno Yakobo anauza anthu a mʼbanja lake ndi onse amene anali naye kuti: “Chotsani milungu yachilendo imene ili pakati panu.+ Dziyeretseni ndipo sinthani zovala zanu. Ekisodo 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musakhale ndi milungu ina iliyonse kupatulapo ine.*+ 1 Akorinto 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho okondedwa anga, pewani* kulambira mafano.+
2 Ndiyeno Yakobo anauza anthu a mʼbanja lake ndi onse amene anali naye kuti: “Chotsani milungu yachilendo imene ili pakati panu.+ Dziyeretseni ndipo sinthani zovala zanu.