Genesis 35:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno Yakobo anauza anthu a mʼbanja lake ndi onse amene anali naye kuti: “Chotsani milungu yachilendo imene ili pakati panu.+ Dziyeretseni ndipo sinthani zovala zanu. Ekisodo 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musakhale ndi milungu ina iliyonse kupatulapo ine.*+ Ekisodo 34:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Samalani kuti musachite pangano ndi anthu okhala mʼdzikomo, chifukwa akamachita uhule ndi milungu yawo komanso kupereka nsembe kwa milungu yawo,+ wina adzakuitanani kunyumba kwake ndipo nanunso mudzadya nsembe yakeyo.+ 1 Akorinto 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho okondedwa anga, pewani* kulambira mafano.+
2 Ndiyeno Yakobo anauza anthu a mʼbanja lake ndi onse amene anali naye kuti: “Chotsani milungu yachilendo imene ili pakati panu.+ Dziyeretseni ndipo sinthani zovala zanu.
15 Samalani kuti musachite pangano ndi anthu okhala mʼdzikomo, chifukwa akamachita uhule ndi milungu yawo komanso kupereka nsembe kwa milungu yawo,+ wina adzakuitanani kunyumba kwake ndipo nanunso mudzadya nsembe yakeyo.+