Yoweli 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Zimenezi zikadzachitika ndidzapereka* mzimu wanga+ kwa chamoyo chilichonse,Ndipo ana anu aamuna ndi ana anu aakazi adzalosera.Amuna achikulire adzalota maloto,Ndipo anyamata adzaona masomphenya.+
28 Zimenezi zikadzachitika ndidzapereka* mzimu wanga+ kwa chamoyo chilichonse,Ndipo ana anu aamuna ndi ana anu aakazi adzalosera.Amuna achikulire adzalota maloto,Ndipo anyamata adzaona masomphenya.+