Mateyu 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Taonani mtumiki wanga+ amene ndamusankha, wokondedwa wanga, amene amandisangalatsa kwambiri.+ Ndidzaika mzimu wanga pa iye+ ndipo anthu a mitundu ina adzawasonyeza bwinobwino chilungamo chenicheni. Mateyu 12:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndithudi, mʼdzina lake mitundu ya anthu idzayembekezera zabwino.”+ Machitidwe 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiponso palibe munthu aliyense amene angatipulumutse, chifukwa palibe dzina lina+ padziko lapansi limene laperekedwa kwa anthu, lomwe lingatipulumutse.”+
18 “Taonani mtumiki wanga+ amene ndamusankha, wokondedwa wanga, amene amandisangalatsa kwambiri.+ Ndidzaika mzimu wanga pa iye+ ndipo anthu a mitundu ina adzawasonyeza bwinobwino chilungamo chenicheni.
12 Ndiponso palibe munthu aliyense amene angatipulumutse, chifukwa palibe dzina lina+ padziko lapansi limene laperekedwa kwa anthu, lomwe lingatipulumutse.”+