1 Akorinto 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma ndikufuna mudziwe kuti mutu wa mwamuna aliyense ndi Khristu.+ Mutu wa mkazi ndi mwamuna+ ndipo mutu wa Khristu ndi Mulungu.+ Aefeso 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Akazi azigonjera amuna awo+ ngati mmene amagonjerera Ambuye, Akolose 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Inu akazi, muzigonjera amuna anu,+ chifukwa zimenezi ndi zoyenera kwa anthu otsatira Ambuye. Tito 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 azikhala oganiza bwino, oyera, ogwira ntchito zapakhomo,* abwino ndiponso ogonjera amuna awo,+ kuti mawu a Mulungu asanyozedwe. 1 Petulo 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mofanana ndi zimenezi, inu akazi muzigonjera amuna anu+ kuti ngati safuna kumvera Mawu a Mulungu, akopeke ndi khalidwe lanu, osati ndi mawu anu+
3 Koma ndikufuna mudziwe kuti mutu wa mwamuna aliyense ndi Khristu.+ Mutu wa mkazi ndi mwamuna+ ndipo mutu wa Khristu ndi Mulungu.+
5 azikhala oganiza bwino, oyera, ogwira ntchito zapakhomo,* abwino ndiponso ogonjera amuna awo,+ kuti mawu a Mulungu asanyozedwe.
3 Mofanana ndi zimenezi, inu akazi muzigonjera amuna anu+ kuti ngati safuna kumvera Mawu a Mulungu, akopeke ndi khalidwe lanu, osati ndi mawu anu+