34 akazi azikhala chete mʼmipingo, chifukwa nʼzosaloleka kuti iwo azilankhula,+ koma azigonjera,+ ngati mmenenso Chilamulo chimanenera. 35 Ngati akufuna kumvetsa zinazake, akafunse amuna awo kunyumba, popeza nʼzochititsa manyazi kuti mkazi azilankhula mumpingo.