Yesaya 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye adzameza* imfa kwamuyaya+Ndipo Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzapukuta misozi pankhope zonse za anthu.+ Adzachotsa kunyozeka kwa anthu ake padziko lonse lapansi,Chifukwa Yehova ndi amene wanena zimenezi. Chivumbulutso 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Wosangalala komanso woyera ndi aliyense amene akuuka nawo pa kuuka koyamba.+ Imfa yachiwiri+ ilibe ulamuliro pa amenewa.+ Koma adzakhala ansembe+ a Mulungu ndi a Khristu, ndipo adzalamulira monga mafumu limodzi ndi Khristu zaka 1,000.+
8 Iye adzameza* imfa kwamuyaya+Ndipo Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzapukuta misozi pankhope zonse za anthu.+ Adzachotsa kunyozeka kwa anthu ake padziko lonse lapansi,Chifukwa Yehova ndi amene wanena zimenezi.
6 Wosangalala komanso woyera ndi aliyense amene akuuka nawo pa kuuka koyamba.+ Imfa yachiwiri+ ilibe ulamuliro pa amenewa.+ Koma adzakhala ansembe+ a Mulungu ndi a Khristu, ndipo adzalamulira monga mafumu limodzi ndi Khristu zaka 1,000.+