Miyambo 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Njira zonse za munthu zimaoneka zabwino kwa iye,+Koma Yehova amafufuza mitima.*+ Aroma 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nanga nʼchifukwa chiyani umaweruza mʼbale wako?+ Kapenanso nʼchifukwa chiyani umanyoza mʼbale wako? Popeza tonse tidzaima patsogolo pa mpando woweruzira wa Mulungu.+ Aheberi 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Palibe cholengedwa chimene Mulungu sangathe kuchiona.+ Chifukwa kwa iye zinthu zonse zili poonekera ndipo amatha kuziona bwinobwino moti ifeyo tidzayankha kwa Mulunguyo pa zochita zathu.+
10 Nanga nʼchifukwa chiyani umaweruza mʼbale wako?+ Kapenanso nʼchifukwa chiyani umanyoza mʼbale wako? Popeza tonse tidzaima patsogolo pa mpando woweruzira wa Mulungu.+
13 Palibe cholengedwa chimene Mulungu sangathe kuchiona.+ Chifukwa kwa iye zinthu zonse zili poonekera ndipo amatha kuziona bwinobwino moti ifeyo tidzayankha kwa Mulunguyo pa zochita zathu.+