1 Petulo 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Muzilemekeza anthu amitundu yonse.+ Muzikonda gulu lonse la abale,+ muziopa Mulungu+ komanso muzilemekeza mfumu.+ 1 Yohane 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ngati wina amanena kuti, “Ndimakonda Mulungu,” koma nʼkumadana ndi mʼbale wake,+ ndiye kuti ndi wabodza. Chifukwa amene sakonda mʼbale wake+ amene amamuona, sangakonde Mulungu amene sanamuonepo.+
17 Muzilemekeza anthu amitundu yonse.+ Muzikonda gulu lonse la abale,+ muziopa Mulungu+ komanso muzilemekeza mfumu.+
20 Ngati wina amanena kuti, “Ndimakonda Mulungu,” koma nʼkumadana ndi mʼbale wake,+ ndiye kuti ndi wabodza. Chifukwa amene sakonda mʼbale wake+ amene amamuona, sangakonde Mulungu amene sanamuonepo.+