Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 23:32, 33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Musamachite pangano ndi iwo kapena milungu yawo.+ 33 Asamakhale mʼdziko lanu kuti asakuchititseni kuti mundichimwire. Mukadzatumikira milungu yawo, udzakhala msampha ndithu kwa inu.”+

  • Deuteronomo 7:3, 4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Musadzachite nawo mgwirizano uliwonse wa ukwati.* Musadzapereke ana anu aakazi kwa ana awo aamuna ndipo musadzatenge ana awo aakazi nʼkuwapereka kwa ana anu aamuna.+ 4 Chifukwa adzachititsa kuti ana anu aamuna asiye kunditsatira ndipo adzatumikira milungu ina.+ Ndiyeno mkwiyo wa Yehova udzakuyakirani ndipo adzakuwonongani mofulumira.+

  • 1 Mafumu 11:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Iye atakalamba,+ akazi akewa anapotoza mtima wake moti Solomo ankatsatira milungu ina+ ndipo sanatumikire Yehova Mulungu wake ndi mtima wathunthu ngati mmene anachitira bambo ake Davide.

  • 1 Akorinto 7:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Mkazi amakhala womangika pa nthawi imene mwamuna wake ali moyo.+ Komano mwamuna wake akamwalira, mkaziyo amakhala womasuka kukwatiwa ndi aliyense amene akufuna, koma akwatiwe mwa Ambuye.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena