Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aroma 15:25, 26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Koma panopa ndatsala pangʼono kupita ku Yerusalemu kukatumikira oyera.+ 26 Abale a ku Makedoniya ndi a ku Akaya apereka mosangalala mphatso kwa oyera ena a ku Yerusalemu omwe ndi osauka.+

  • 1 Akorinto 16:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pa nkhani ya zopereka zopita kwa oyerawo,+ mukhoza kutsatira malangizo amene ndinapereka ku mipingo ya ku Galatiya.

  • 2 Akorinto 9:1, 2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ponena za utumiki wothandiza oyerawo,+ nʼzosafunika kuti ndichite kukulemberani. 2 Chifukwa ndikudziwa kuti muli ndi mtima wofunitsitsa ndipo ndikunena zimenezi monyadira kwa anthu a ku Makedoniya. Ndikumawauza kuti abale a ku Akaya akhala okonzeka kwa chaka chimodzi tsopano, ndipo kudzipereka kwanu kwalimbikitsa abale ambiri kumeneko.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena