Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 4:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndiponso palibe munthu aliyense amene angatipulumutse, chifukwa palibe dzina lina+ padziko lapansi limene laperekedwa kwa anthu, lomwe lingatipulumutse.”+

  • Aefeso 1:20, 21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 pamene anazigwiritsa ntchito poukitsa Khristu kwa akufa nʼkumukhazika kudzanja lake lamanja+ mʼmalo akumwamba. 21 Anamuika pamwamba kuposa boma lililonse, ulamuliro uliwonse, anthu amphamvu onse, ambuye onse, ndi aliyense amene ali ndi dzina laulemu,+ osati mu nthawi* ino yokha, komanso imene ikubwerayo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena