3 Pa zinthu zoyambirira zimene ndinakuphunzitsani, zomwenso ineyo ndinalandira, panali zonena kuti, Khristu anafera machimo athu, mogwirizana ndi Malemba.+ 4 Ndiponso kuti anaikidwa mʼmanda,+ kenako anaukitsidwa+ pa tsiku lachitatu,+ mogwirizana ndi Malemba.+