Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 22:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndiyeno Hananiya, munthu woopa Mulungu mogwirizana ndi Chilamulo, amene anali ndi mbiri yabwino pakati pa Ayuda onse akumeneko,

  • 1 Atesalonika 4:11, 12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Muziyesetsa kukhala mwamtendere,+ musamalowerere nkhani za ena+ ndipo muzigwira ntchito ndi manja anu+ mogwirizana ndi malangizo amene tinakupatsani. 12 Muzichita zimenezi kuti mukhale ndi makhalidwe amene angachititse kuti anthu akunja azikulemekezani+ ndiponso kuti mukhale osasowa kanthu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena