-
1 Timoteyo 6:3, 4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ngati munthu akuphunzitsa zinthu zabodza, ndipo sakuvomereza malangizo abwino+ ochokera kwa Ambuye wathu Yesu Khristu, ndiponso zinthu zimene timaphunzira zogwirizana ndi kudzipereka kwathu kwa Mulungu,+ 4 munthu ameneyo ndi wodzitukumula ndiponso wonyada ndipo samvetsa kalikonse.+ Mʼmalomwake, amakonda kukangana ndiponso kutsutsana pa mawu.+ Zimenezi zimayambitsa nsanje, mikangano, kunenerana mawu achipongwe* ndiponso kuganizirana zoipa.
-