Yohane 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yesu anayankha kuti: “Ndithudi ndikukuuza, munthu sangathe kulowa mu Ufumu wa Mulungu ngati atapanda kubadwa mwa madzi+ ndi mzimu.+ Aroma 8:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Komatu si zokhazi. Ifeyo amene tili ndi zipatso zoyambirira zomwe ndi mzimu, tikubuula mumtima mwathu+ pamene tikudikira ndi mtima wonse kuti Mulungu atitenge kukhala ana ake,+ kutimasula ndi dipo* ku matupi athuwa. 2 Akorinto 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiye ngati aliyense ali wogwirizana ndi Khristu, iye ndi cholengedwa chatsopano.+ Zinthu zakale zinatha, ndipo pali zatsopano.
5 Yesu anayankha kuti: “Ndithudi ndikukuuza, munthu sangathe kulowa mu Ufumu wa Mulungu ngati atapanda kubadwa mwa madzi+ ndi mzimu.+
23 Komatu si zokhazi. Ifeyo amene tili ndi zipatso zoyambirira zomwe ndi mzimu, tikubuula mumtima mwathu+ pamene tikudikira ndi mtima wonse kuti Mulungu atitenge kukhala ana ake,+ kutimasula ndi dipo* ku matupi athuwa.
17 Ndiye ngati aliyense ali wogwirizana ndi Khristu, iye ndi cholengedwa chatsopano.+ Zinthu zakale zinatha, ndipo pali zatsopano.