6 Koma Yesu walandira utumiki wapamwamba kwambiri, chifukwa iyenso ndi mkhalapakati+ wa pangano labwino kwambiri,+ limene lakhazikitsidwa mwalamulo pa malonjezo abwinonso.+
15 Ndiye chifukwa chake iye ndi mkhalapakati wa pangano latsopano+ kuti anthu amene aitanidwa alandire lonjezo la moyo wosatha.+ Izi zatheka chifukwa cha imfa yake, imene inali ngati dipo lowamasula+ ku machimo amene iwo anali nawo mʼpangano lakale lija.