Levitiko 16:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Limeneli likhale lamulo kwa inu mpaka kalekale,+ kuti machimo onse a Aisiraeli aziphimbidwa kamodzi pa chaka.”+ Choncho iye anachita mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.
34 Limeneli likhale lamulo kwa inu mpaka kalekale,+ kuti machimo onse a Aisiraeli aziphimbidwa kamodzi pa chaka.”+ Choncho iye anachita mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.