Aheberi 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho malamulo oyambawo akuchotsedwa chifukwa ndi operewera komanso osathandiza.+ Aheberi 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Popeza Chilamulo chimangochitira chithunzi+ zinthu zabwino zimene zikubwera+ ndipo si zinthu zenizenizo, sichingachititse* amene amalambira Mulungu kukhala angwiro pogwiritsa ntchito nsembe zimene amapereka mosalekeza chaka chilichonse.+
10 Popeza Chilamulo chimangochitira chithunzi+ zinthu zabwino zimene zikubwera+ ndipo si zinthu zenizenizo, sichingachititse* amene amalambira Mulungu kukhala angwiro pogwiritsa ntchito nsembe zimene amapereka mosalekeza chaka chilichonse.+