Oweruza 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Amidiyani ndi Aamaleki pamodzi ndi anthu onse a Kumʼmawa+ anadzaza mʼchigwa chonse chifukwa anali ambiri ngati dzombe. Ngamila zawo zinali zosawerengeka,+ zambiri ngati mchenga wa mʼmbali mwa nyanja. Oweruza 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Amuna 300 aja anapitiriza kuliza malipenga, ndipo Yehova anachititsa Amidiyani kuukirana okhaokha mumsasa wonsewo.+ Asilikaliwo anathawa mpaka kukafika ku Beti-sita ndi ku Zerera mpaka kumalire kwa mzinda wa Abele-mehola+ pafupi ndi Tabati.
12 Amidiyani ndi Aamaleki pamodzi ndi anthu onse a Kumʼmawa+ anadzaza mʼchigwa chonse chifukwa anali ambiri ngati dzombe. Ngamila zawo zinali zosawerengeka,+ zambiri ngati mchenga wa mʼmbali mwa nyanja.
22 Amuna 300 aja anapitiriza kuliza malipenga, ndipo Yehova anachititsa Amidiyani kuukirana okhaokha mumsasa wonsewo.+ Asilikaliwo anathawa mpaka kukafika ku Beti-sita ndi ku Zerera mpaka kumalire kwa mzinda wa Abele-mehola+ pafupi ndi Tabati.