Ekisodo 16:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Aisiraeli anadya mana kwa zaka 40+ mpaka pamene analowa mʼdziko limene munkakhala anthu.+ Iwo ankadya mana mpaka pamene anafika mʼmalire a dziko la Kanani.+ Numeri 32:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova anawakwiyira koopsa Aisiraeli ndipo anawachititsa kuti azingoyendayenda mʼchipululu kwa zaka 40,+ mpaka mʼbadwo wonse wochita zoipa pamaso pa Yehova utatha.+ Salimo 95:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamene makolo anu anandiyesa.+Iwo anatsutsana ndi ine ngakhale kuti anaona ntchito zanga.+
35 Aisiraeli anadya mana kwa zaka 40+ mpaka pamene analowa mʼdziko limene munkakhala anthu.+ Iwo ankadya mana mpaka pamene anafika mʼmalire a dziko la Kanani.+
13 Yehova anawakwiyira koopsa Aisiraeli ndipo anawachititsa kuti azingoyendayenda mʼchipululu kwa zaka 40,+ mpaka mʼbadwo wonse wochita zoipa pamaso pa Yehova utatha.+