2 Akorinto 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pomaliza abale, pitirizani kusangalala, kusintha maganizo, kulimbikitsidwa,+ kukhala ndi maganizo ogwirizana+ ndiponso kukhala mwamtendere.+ Mukatero, Mulungu amene ndi wachikondi komanso wamtendere+ adzakhala nanu. 1 Atesalonika 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Muziwasonyeza chikondi komanso ulemu waukulu chifukwa cha ntchito yawo.+ Muzikhala mwamtendere pakati panu.+ 2 Petulo 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho okondedwa, popeza mukuyembekezera zinthu zimenezi, yesetsani kuchita zonse zimene mungathe kuti Mulungu adzakupezeni muli oyera, opanda cholakwa ndiponso muli mumtendere.+
11 Pomaliza abale, pitirizani kusangalala, kusintha maganizo, kulimbikitsidwa,+ kukhala ndi maganizo ogwirizana+ ndiponso kukhala mwamtendere.+ Mukatero, Mulungu amene ndi wachikondi komanso wamtendere+ adzakhala nanu.
13 Muziwasonyeza chikondi komanso ulemu waukulu chifukwa cha ntchito yawo.+ Muzikhala mwamtendere pakati panu.+
14 Choncho okondedwa, popeza mukuyembekezera zinthu zimenezi, yesetsani kuchita zonse zimene mungathe kuti Mulungu adzakupezeni muli oyera, opanda cholakwa ndiponso muli mumtendere.+