Chivumbulutso 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako ndinayangʼana ndipo ndinaona Mwanawankhosa+ ataimirira paphiri la Ziyoni.+ Iye anali limodzi ndi enanso 144,000+ amene analembedwa dzina lake ndi dzina la Atate+ wake pazipumi zawo. Chivumbulutso 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Maso ake anali ngati lawi la moto+ ndipo pamutu pake panali zisoti zachifumu zambiri. Iye analembedwa dzina limene palibe wina aliyense amene akulidziwa koma iye yekha.
14 Kenako ndinayangʼana ndipo ndinaona Mwanawankhosa+ ataimirira paphiri la Ziyoni.+ Iye anali limodzi ndi enanso 144,000+ amene analembedwa dzina lake ndi dzina la Atate+ wake pazipumi zawo.
12 Maso ake anali ngati lawi la moto+ ndipo pamutu pake panali zisoti zachifumu zambiri. Iye analembedwa dzina limene palibe wina aliyense amene akulidziwa koma iye yekha.