Yohane 16:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ine ndakuuzani zimenezi kuti mukhale mu mtendere chifukwa cha ine.+ Mʼdzikomu mukumana ndi mavuto aakulu, koma limbani mtima. Ine ndaligonjetsa dziko.”+
33 Ine ndakuuzani zimenezi kuti mukhale mu mtendere chifukwa cha ine.+ Mʼdzikomu mukumana ndi mavuto aakulu, koma limbani mtima. Ine ndaligonjetsa dziko.”+