Salimo 33:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Muimbireni nyimbo yatsopano.+Imbani mwaluso choimbira cha zingwe ndipo muzifuula mosangalala. Salimo 144:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu Mulungu, ine ndidzakuimbirani nyimbo yatsopano.+ Ndidzaimba nyimbo zokutamandani ndi choimbira cha zingwe 10. Yesaya 42:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Imbirani Yehova nyimbo yatsopano.+Mʼtamandeni kuchokera kumalekezero a dziko lapansi,+Inu nonse amene mumadalira nyanja komanso zonse zimene zimakhala mmenemo,Inu zilumba ndi anthu amene amakhala mʼzilumbazo.+ Chivumbulutso 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo ankaimba nyimbo imene inkamveka ngati nyimbo yatsopano+ pamaso pa mpando wachifumu, pamaso pa angelo 4+ ndi pamaso pa akulu.+ Palibe amene anatha kuphunzira nyimboyo kupatulapo 144,000+ amene anagulidwa padziko lapansi.
9 Inu Mulungu, ine ndidzakuimbirani nyimbo yatsopano.+ Ndidzaimba nyimbo zokutamandani ndi choimbira cha zingwe 10. Yesaya 42:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Imbirani Yehova nyimbo yatsopano.+Mʼtamandeni kuchokera kumalekezero a dziko lapansi,+Inu nonse amene mumadalira nyanja komanso zonse zimene zimakhala mmenemo,Inu zilumba ndi anthu amene amakhala mʼzilumbazo.+ Chivumbulutso 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo ankaimba nyimbo imene inkamveka ngati nyimbo yatsopano+ pamaso pa mpando wachifumu, pamaso pa angelo 4+ ndi pamaso pa akulu.+ Palibe amene anatha kuphunzira nyimboyo kupatulapo 144,000+ amene anagulidwa padziko lapansi.
10 Imbirani Yehova nyimbo yatsopano.+Mʼtamandeni kuchokera kumalekezero a dziko lapansi,+Inu nonse amene mumadalira nyanja komanso zonse zimene zimakhala mmenemo,Inu zilumba ndi anthu amene amakhala mʼzilumbazo.+
3 Iwo ankaimba nyimbo imene inkamveka ngati nyimbo yatsopano+ pamaso pa mpando wachifumu, pamaso pa angelo 4+ ndi pamaso pa akulu.+ Palibe amene anatha kuphunzira nyimboyo kupatulapo 144,000+ amene anagulidwa padziko lapansi.