Mateyu 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthu onse adzadana nanu chifukwa cha dzina langa,+ koma amene adzapirire* mpaka mapeto ndi amene adzapulumuke.+ 2 Timoteyo 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tikapitiriza kupirira, tidzalamuliranso naye monga mafumu.+ Tikamukana, iyenso adzatikana,+
22 Anthu onse adzadana nanu chifukwa cha dzina langa,+ koma amene adzapirire* mpaka mapeto ndi amene adzapulumuke.+