Mateyu 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako anthu adzakuperekani kuti mukazunzidwe+ ndipo adzakuphani.+ Anthu a mitundu yonse adzadana nanu chifukwa cha dzina langa.+
9 Kenako anthu adzakuperekani kuti mukazunzidwe+ ndipo adzakuphani.+ Anthu a mitundu yonse adzadana nanu chifukwa cha dzina langa.+