Mateyu 25:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Anthu amenewa adzachoka kupita kuchiwonongeko chosatha,*+ koma olungama kumoyo wosatha.”+ 2 Atesalonika 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anthu amenewa adzawaweruza kuti alandire chilango cha chiwonongeko chamuyaya+ ndipo adzachotsedwa pamaso pa Ambuye moti sadzaonanso mphamvu zake zaulemerero. Chivumbulutso 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nthawi yomweyo, ananenanso kachiwiri kuti: “Tamandani Ya!*+ Utsi umene ukufuka chifukwa cha kuwotchedwa kwake udzafuka mpaka kalekale.”+
9 Anthu amenewa adzawaweruza kuti alandire chilango cha chiwonongeko chamuyaya+ ndipo adzachotsedwa pamaso pa Ambuye moti sadzaonanso mphamvu zake zaulemerero.
3 Nthawi yomweyo, ananenanso kachiwiri kuti: “Tamandani Ya!*+ Utsi umene ukufuka chifukwa cha kuwotchedwa kwake udzafuka mpaka kalekale.”+