Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Atesalonika 1
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Zimene Zili Mʼbuku la 2 Atesalonika

      • Moni (1, 2)

      • Chikhulupiriro cha Atesalonika chinkakulirakulira (3-5)

      • Anthu osamvera adzalandira chilango (6-10)

      • Ankapempherera mpingo (11, 12)

2 Atesalonika 1:1

Mawu a M'munsi

  • *

    Amene amadziwikanso kuti Sila.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ak 1:19

2 Atesalonika 1:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1At 3:12; 4:9, 10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2005, tsa. 32

2 Atesalonika 1:4

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “masautso.”

  • *

    Kapena kuti, “mukuwapirira.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1At 2:19
  • +1At 1:6; 2:14; 1Pe 2:21

2 Atesalonika 1:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 14:22; Aro 8:17; 2Ti 2:12

2 Atesalonika 1:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 12:19; Chv 6:9, 10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 33

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2004, tsa. 19

2 Atesalonika 1:7

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “adzaululike.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Lu 17:29, 30; 1Pe 1:7
  • +Mko 8:38

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2004, tsa. 19

    5/1/1993, tsa. 22

2 Atesalonika 1:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 2:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 33

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    9/2019, ptsa. 12-13

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2004, tsa. 19

    5/1/1993, tsa. 22

    5/1/1989, tsa. 19

    1/1/1989, tsa. 20

2 Atesalonika 1:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Pe 3:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    5/1/1989, tsa. 19

    Kukambitsirana, tsa. 147

2 Atesalonika 1:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 8:30

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

2 Ates. 1:12Ak 1:19
2 Ates. 1:31At 3:12; 4:9, 10
2 Ates. 1:41At 2:19
2 Ates. 1:41At 1:6; 2:14; 1Pe 2:21
2 Ates. 1:5Mac 14:22; Aro 8:17; 2Ti 2:12
2 Ates. 1:6Aro 12:19; Chv 6:9, 10
2 Ates. 1:7Lu 17:29, 30; 1Pe 1:7
2 Ates. 1:7Mko 8:38
2 Ates. 1:8Aro 2:8
2 Ates. 1:92Pe 3:7
2 Ates. 1:11Aro 8:30
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
2 Atesalonika 1:1-12

Kalata Yachiwiri Yopita kwa Atesalonika

1 Ine Paulo ndili limodzi ndi Silivano* komanso Timoteyo+ ndipo ndikulembera mpingo wa Atesalonika, womwe ndi wogwirizana ndi Mulungu Atate wathu komanso Ambuye Yesu Khristu kuti:

2 Kukoma mtima kwakukulu komanso mtendere wochokera kwa Mulungu Atate ndi Ambuye Yesu Khristu, zikhale nanu.

3 Tikuyenera kumathokoza Mulungu nthawi zonse chifukwa cha inu abale. Zimenezi nʼzoyenera chifukwa chikhulupiriro chanu chikukula kwambiri ndipo chikondi chimene aliyense amasonyeza kwa mnzake chikuwonjezereka.+ 4 Choncho ifeyo timanyadira+ tikamanena za inu ku mipingo ya Mulungu chifukwa cha kupirira kwanu ndi chikhulupiriro chimene mumasonyeza mukamazunzidwa komanso kulimbana ndi mavuto* amene mukukumana nawo.*+ 5 Umenewu ndi umboni wakuti Mulungu amaweruza molungama ndipo chifukwa cha zimenezi mwaonedwa kuti ndinu oyenerera Ufumu wa Mulungu, umene mukuuvutikira.+

6 Popeza Mulungu ndi wolungama, iye adzapereka chilango kwa amene amachititsa kuti muzizunzika.+ 7 Koma inu amene mukuvutika mudzapatsidwa mpumulo pamodzi ndi ife pa nthawi imene Ambuye Yesu adzaonekere*+ kuchokera kumwamba limodzi ndi angelo ake amphamvu+ 8 mʼmoto walawilawi. Pa nthawi imeneyo adzabwezera chilango kwa anthu osadziwa Mulungu komanso kwa anthu amene samvera uthenga wabwino wonena za Ambuye wathu Yesu.+ 9 Anthu amenewa adzawaweruza kuti alandire chilango cha chiwonongeko chamuyaya+ ndipo adzachotsedwa pamaso pa Ambuye moti sadzaonanso mphamvu zake zaulemerero. 10 Zimenezi zidzachitika pa nthawi imene adzabwere kudzalandira ulemerero limodzi ndi oyera ake. Pa tsiku limenelo, onse amene anamukhulupirira adzamuyangʼanitsitsa mwachidwi, chifukwa munakhulupirira umboni umene tinapereka kwa inu.

11 Pa chifukwa chimenechi, timakupemphererani nthawi zonse kuti Mulungu wathu akuoneni kuti ndinu oyenereradi kuitanidwa ndi iye.+ Mulungu achite mokwanira zinthu zonse zabwino zimene akufuna kuchita ndi mphamvu zake, ndipo achititse kuti ntchito zanu zachikhulupiriro zikhale zopindulitsa. 12 Timakupemphererani kuti dzina la Ambuye wathu Yesu lilemekezeke mwa inu komanso kuti inu mulemekezeke mwa iye, mogwirizana ndi kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu wathu ndi kwa Ambuye Yesu Khristu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena