Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • nwt tsamba 2194-2195
  • A6-B Tchati: Aneneri Komanso Mafumu a Yuda ndi Isiraeli (Gawo 2)

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • A6-B Tchati: Aneneri Komanso Mafumu a Yuda ndi Isiraeli (Gawo 2)
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • Mafumu a mu Ufumu Wakumʼmwera (Kupitiriza)
  • Mafumu a mu Ufumu Wakumpoto (Kupitiriza)
  • Mmene Mungapezere Malemba M’Baibulo Lanu
    Nkhani Zina
  • Aneneri Amene Uthenga Wawo Ungatithandize
    Muzikumbukira Tsiku la Yehova Nthawi Zonse
  • Kutumikira Mulungu “M’masiku Otsiriza”
    Zimene Mulungu Akutiuza Kudzera mwa Yeremiya
  • Moyo wa Ezekieli Komanso Mmene Zinthu Zinalili M’nthawi Yake
    Yehova Wabwezeretsa Kulambira Koyera
Onani Zambiri
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
A6-B Tchati: Aneneri Komanso Mafumu a Yuda ndi Isiraeli (Gawo 2)

A6-B

Tchati: Aneneri Komanso Mafumu a Yuda ndi Isiraeli (Gawo 2)

Losindikizidwa

Mafumu a mu Ufumu Wakumʼmwera (Kupitiriza)

777 B.C.E.

Yotamu: zaka 16

762

Ahazi: zaka 16

746

Hezekiya: zaka 29

716

Manase: zaka 55

661

Amoni: zaka ziwiri

659

Yosiya: zaka 31

628

Yehoahazi: miyezi itatu

Yehoyakimu: zaka 11

618

Yehoyakini: miyezi itatu ndi masiku 10

617

Zedekiya: zaka 11

607

Magulu ankhondo a ku Babulo anawononga Yerusalemu ndi kachisi wake motsogoleredwa ndi Nebukadinezara. Zedekiya, mfumu yomaliza yochokera mumzere wa Davide, inachotsedwa pampando

Mafumu a mu Ufumu Wakumpoto (Kupitiriza)

c. 803 B.C.E.

Zekariya: analamulira kwa miyezi 6 yokha

Tinganene kuti Zekariya anayamba kulamulira, koma zinali zisanatsimikizirike kuti ufumuwo ndi wake mpaka cha mʼma 792

c. 791

Salumu: mwezi umodzi

Menahemu: zaka 10

c. 780

Pekahiya: zaka ziwiri

c. 778

Peka: zaka 20

c. 758

Hoshiya: zaka 9 kuchokera cha mʼma 748

c. 748

Zikuoneka kuti ufumu wa Hoshiya unakhazikika kapena nʼkutheka kuti ankathandizidwa ndi mfumu ya Asuri dzina lake Tigilati-pilesere Wachitatu cha mʼma 748

740

Asuri analanda Samariya, nʼkuyamba kulamulira Aisiraeli; ufumu wa mafuko 10 wa Isiraeli unatha

  • Mayina a Aneneri

  • Yesaya

  • Mika

  • Zefaniya

  • Yeremiya

  • Nahumu

  • Habakuku

  • Danieli

  • Ezekieli

  • Obadiya

  • Hoseya

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena