Zisonyezero za Voliyamu 31 ya “Galamukani!”
ACHICHEPERE AKUFUNSA KUTI . . .
Kodi Baibulo Nloyenerera kwa Ine? 2/8
Kodi Cholakwika Nchiyani ndi Kukhala ndi Nthaŵi Yabwino? 4/8
Kodi Cholakwika Nchiyani ndi Kulimba Mtima? 2/8
Kodi Kuseka Kogwira Ntchito Sikuli Chabe Chiphwete Chosavulaza? 7/8
Kodi Nchifukwa Ninji Achikulire Samandimvetsetsa? 4/8
Kodi Nchifukwa Ninji Amayi Samapezeka Pamene Ndifika Panyumba? 3/8
Kodi Ndimotani Mmene Ndingachirire ku Kugwiritsira Ntchito Molakwa Mankhwala Ogodomalitsa? 5/8
Kodi Ndimotani Mmene Ndingathandizire Achikulire Kundimvetsetsa? 5/8
Kodi Ndingalamulire Motani Kupsya Mtima Kwanga? 10/8
Kodi Ndingalimbane Ndi Kupsyinjika? 8/8
Kodi Ndingapeze Bwanji Chisangalalo Monga Mwana Yekha? 11/8
Kodi Ndingaphunzire Motani Pamene Mphunzitsi Wanga Ali Wogwetsa Ulesi Chotero? 1/8
Kodi Ndiyenera Kutsatira Machitachita Aposachedwapa? 6/8
Kodi Sitingathe Kukhala Mabwenzi Chabe? 1/8
Makolo Anga Amagwira Ntchito—Kodi Ndingachitenji Ndekha M’nyumba Yopanda Kanthu? 6/8
Nchifukwa Ninji Ndimapsya Mtima? 9/8
Nchiyani Chimandipangitsa Kudzimva Wosungulumwa Chotero? 12/8
CHIPEMBEDZO
Baibulo Kodi Kapena Mwambo?—Chothetsa Nzeru kwa Akatolika Owona Mtima 3/8
Chigumula Ndi Chirala—Kodi Ndizochita za Mulungu? 3/8
Chipembedzo mu Ndale Zadziko—Kodi Ichi Chiri Chifuno cha Mulungu? 9/8
Chowonadi Ponena za Miyambo ya Isitala 4/8
Kodi Matsoka ali “Zochita za Mulungu?” 6/8
Kukhulupirika kwa Masiku a Baibulo Nkosatsutsika 7/8
‘Manja Anu Adzaza ndi Mwazi’ 12/8
Mawonekedwe Osiyanasiyana a Isitala 3/8
‘Mwenzi Onse Atakhala Aneneri!’ 3/8
Nchifukwa Ninji Atsogoleri Achipembedzo Amasanganizira mu Ndale Zadziko? 9/8
Nsanja ya Babele Yamakono? 12/8
Silirinso Bukhu Loletsedwa 3/8
UMOYO NDI MANKHWALA
AIDS, Kuthiriridwa Mwazi, ndi Mboni za Yehova 1/8
Bwanji Ponena za Umoyo Wabwino wa Inu Eni? 10/8
Kensa—Kodi Tikuchita Motani? 4/8
“Kensa—Ndikuigonjetsa” 4/8
Kodi Mungagonjetse Kensa? Kodi Choichititsa Nchiyani? 4/8
Kodi Mungagonjetse Kensa? 4/8
Kuchiritsa Kosatha Kuli Pafupi 10/8
Kuchotsa Mimba—Chidziŵitso Chidzetsa Thayo 8/8
Kuchotsa Mimba—Dziko Logawanika 8/8
Kuchotsa Mimba—Kodi Ndani ali Wokhoza? 8/8
Kuchotsa Mimba—Ndi Magwero a Moyo 8/8
Kuchotsa Mimba—Pa Mtengo Wapatali 8/8
Kudwala Maganizo—Kodi Pali Kuchiritsa Kuli Konse? 7/8
Kudwala Maganizo—Nthenda ya Chinsinsi 7/8
Kusakaza Kokulira kwa Fodya mu Greece 10/8
“Ngwazi ya Nkhokera” 10/8
Pamene Kensa Idzaleka 4/8
Sammy Wamng’onoyo Anaphedwa ndi AIDS! 2/8
Thanzi Labwino M’chikho cha Madzi! 1/8
CHUMA NDI NTCHITO YOLEMBEDWA
Akazi Ogwira Ntchito—Mmene Maiko Osatukuka Amawonera 2/8
LINGALIRO LABAIBULO
Kodi Helo Ngwotentha? 6/8
Kodi Kukhulupirira Malaulo Kuli Kosavulaza? 10/8
Kodi Mulungu Anali ndi Chiyambi? 2/8
Kulankhula M’malirime—Kodi Nkochokera kwa Mulungu? 8/8
Ndani Angatonthoze ‘Kulira kwa Njala’? 12/8
MAIKO NDI ANTHU
Akasupe a Moto ku Hawaii 10/8
Chipwirikiti mu South Africa 4/8
Dziko Losagwirizana—Kodi Chothetsera Nchiyani? 4/8
Kodi Kunayambira Kuti? 8/8
Mtendere, Chigwirizano, ndi Chikondi Pakati pa Kusakhazikika kwa Zinthu 3/8
MAUNANSI A ANTHU
Bongo Wodabwitsa Umenewu wa Khanda 11/8
Chisonkhezero Kaamba ka Mphamvu za Nzeru Zozizwitsa 11/8
Kodi Nkukwatiriranji? 5/8
Kuchokera ku Chikuta Kufika ku Manda—Chosowa Chathu Chachikulu Ndi Chikondi 7/8
Kukhalira Limodzi Kapena Ukwati? 5/8
Machitachita Owonjezereka ku Ukwati—Kulekeranji? 5/8
Njira ya Moyo ya Ogonana Ofanana Ziwalo—Kodi Iri Yamoyo Kwambiri Motani? 1/8
Phunzitsani Mwana Wanu m’Njira Yabwino—Ndipo Kuchiteni Kuchokera ku Ukhanda! 11/8
Ukwati—Ngwoyenerera? 5/8
Umoyo Wabwino Kaamba ka Mtundu Wonse wa Anthu—Liti? 10/8
MBONI ZA YEHOVA
Chitonthozo kwa Wolapa 6/8
“Kulankhula za Kugwirira Ntchito Pamodzi” 8/8
Kupeza Gulu la Nkhondo Labwino 9/8
Ndinamva Dzina la Mulungu ndi Kuiwala la Mwinine 5/8
Ndiri Woyamikira ndi Zimene Ndiri Nazo 10/8
Ntchito ya Magazini ku Japan Ibwera ‘Mu Dongosolo’ 9/8
Omaliza Maphunziro a Gileadi Akudziika Pansi pa Chitsogozo cha Mulungu 3/8
Trinidad Akuimanga m’Masiku Anayi! 1/8
“Tsopano Udzafa!” 1/8
Ziŵanda Zindiposa Mphamvu 6/8
NKHANI ZOSIYANASIYANA
Allan Kardec—Ngwazi ya Kukhulupirira Mizimu 11/8
Kodi Chothetsera Nchiyani? 3/8
Kodi Mungatseke Danga la Mbadwo? 5/8
Kupambutsira Ndege ku Malta—Koma Ndinapulumuka 3/8
Kupenda Nyenyezi—Kodi Ndimaseŵera Osavulaza? 2/8
Kupenda Nyenyezi Kuyambanso! 2/8
Mbala Yosankha 3/8
Mtsogolo Mwanu—Kodi Munalembedwa m’Nyenyezi? 2/8
NYAMA NDI ZOMERA
Katungulume—Zipatso Zonga Ntedza 9/8
Khalani ndi Moyo Kuti Mudzawone Nkhalango Zikusangalala 12/8
Kodi Nkhalango Zingasungidwe? 12/8
Kumanani ndi Kasenye Kakang’ono Koposa m’Dziko 10/8
Mvula ya m’Nyengo Yachisanu Imabweretsa Maluŵa a m’Chipululu—Ndiponso Zosungira za Zomera Zomadzazanso 11/8
“Ndidyeni Ngati Mulibe Mantha” 11/8
SAYANSI
Koloko ya Radiocarbon 7/8
Kulankhula ndi Kupenya Kupyolera m’Galasi 11/8
Masiku a Usayansi a Nthaŵi Zakale 7/8
Maso m’Mlengalenga 9/8
ZOCHITIKA ZADZIKO NDI MIKHALIDWE
Bombalo ndi Mtsogolo mwa Munthu 2/8
Chida Chankhondo Chotsirizira ndi Kulimbanira Chisungiko 2/8
Chigwirizano cha Mitundu Chidzandira ku Imfa Yake 10/8
Chigwirizano cha Mitundu, Chosonkhezeredwa ndi Mantha 11/8
‘Kamodzi Koyambira Ulendo’ 1/8
Kodi Nchiyani Chachitika ku Nthaka Yathu? 7/8
Kufunafuna Chisungiko m’Mbadwo wa Bomba 2/8
Kumwa ndi Kuyendetsa Galimoto—Kodi Nchiyani Chimene Chingachitidwe? 1/8
Kupsyinjika kwa Dziko Lapansi Ndipo ku Nkhondo Kachiŵirinso 9/8
Maseŵera a Chihuligani—Kodi Ndi Nthenda Kapena Chizindikiro? 1/8
Nkhondo ya Dziko II—Kutha Kwake Kowopsya ndi Kwamoto 12/8
Uchigawenga—Kodi Aliyense Ngwotetezereka? 3/8
Zaka za m’Makumi Aŵiri Zobangula—Zikhala Bata Pamaso pa Namondwe 8/8
Zoledzeretsa ndi Inu 1/8
Zoledzeretsa ndi Kuyendetsa Galimoto 1/8