Zisonyezero za Volyumu 33 ya Galamukani!
ACHICHEPERE AKUFUNSA KUTI . . .
Kodi Angachitirenji Motero kwa Ine? 11/8
Kujeda, 7/8, 8/8
Kukambitsirana, 6/8
Kukhalabe Mabwenzi, 10/8
Kukhala Chitsanzo kwa Achichepere? 11/8
Kumenyana kwa Makolo, 12/8
Kunyada kwa Ufuko, 2/8
Kupalana Ubwenzi Kwachipambano, 3/8, 5/8
Kusamalira Ndalama Zanga, 1/8
Kusankha Zovala, 10/8
Kutukwana, 9/8
Ntchito, 2/8
Nyimbo Zachikondi, 7/8
Ovutitsa Kusukulu, 8/8
Wokonzekera Kuyendetsa? 3/8, 4/8
CHIPEMBEDZO
Bwalo Lankhondo la Milungu, 2/8
Chihindu—Dzina Lanu Liri Kulekerera, 4/8
Chipembedzo Chofunikira Kukonzanso, 9/8
Chipembedzo—Chonyenga Cholakidwa ndi Nthaŵi Yake Yapita! 12/8
Chiprotesitanti—Kodi Chinali Kukonzanso? 9/8
Chiwunikiro Chomwe Chinalonjeza Ufulu (Chibuda), 5/8
‘Choloŵetsedwa m’Kugwa Kokulira Kwa Makhalidwe Abwino,’ 1/8
Dziko Lachikristu Lilimbana ndi Kusintha Kwadziko, 10/8
Kodi Apapa Samalakwa? 2/8
Kubwezeretsedwa Kuyandika! 11/8
Kuchokera Mu Mdima, Chinachake “Choyera,” 7/8
Kuchotsa Kuunika kwa Uthenga Wabwino, 7/8
Kudikirirabe Mesiya, 6/8
Kufufuza kwa Kum’mawa kaamba ka Njira Yolondola, 4/8
Kugonjera ku Chifuniro cha Mulungu (Chisilamu), 8/8
Kusagwirizana Kwa Chipembedzo—Mmene Kunayambira, 1/8
Kutembenukira ku Lupanga, 8/8
Kuyang’ana Kosamalitsa pa Chipembedzo, 1/8
Milungu ya Nthanthi Yopanda Phindu, 3/8
Mpalu, Nsanja, ndi Inu! 2/8
Mtundu Woikidwa Pambali (Israyeli), 3/8
Njira ya Chikhulupiriro, Chiyembekezo, ndi Chikondi (Chikristu), 6/8
Njira Zopeŵera Kutenga Mimba—Kodi Ndani Ayenera Kusankha? 10/8
Nthaŵi Yoŵerengera Yayandikira, 12/8
Pamene “Akristu” ndi “Akunja” Anakumana, 10/8
Zogulidwa Kwambiri za Chipembedzo (Mabukhu Opatulika), 4/8
Zovala Zokhathamira ndi Mwazi, 11/8
Zozizwitsa ndi Masomphenya, 3/8
CHUMA NDI NTCHITO YOLEMBEDWA
Kubwezeretsa Chuma, 5/8
Vuto la Mtengo wa Kakhalidwe, 5/8
LINGALIRO LABAIBULO
Kodi Kulambira Makolo Kuli Kwachikristu? 3/8
Kodi Muyenera Kuwopa Diso Lankhwezule? 2/8
Kodi Wochita Kugonana kwa Ofanana Ziŵalo Angakhale Mtumiki wa Mulungu? 8/8
Kugonana kwa Ofanana Ziŵalo—Kodi Nchiyani Chimene Chiri Thayo la Atsogoleri Achipembedzo? 9/8
Kugonana kwa Ofanana Ziwalo—Nkulekeranji? 7/8
Kusuta—Maupanduwo, 11/8
Nchiyani Chomwe Chiri Chifuno cha Moyo? 2/8
MAIKO NDI ANTHU
Kuthetsa Mavuto a Osauka, 1/8
Tchalitchi m’Ndale Zadziko (Brazil), 1/8
MBONI ZA YEHOVA
Kuchilikizidwa ndi Chiyembekezo cha Ufumu, 11/8
Kuchokera ku Mpandu Kukhala Mkristu, 10/8
Nthanthi Yonena Zaumulungu Siiri Kaamba ka Ine (A. Monteiro Carneiro), 1/8
“Sitipatsa Mlandu Mulungu,” 8/8
Sitolo Yochedwetsedwa, 8/8
NKHANI ZOSIYANASIYANA
Kugwirira Chigololo—Anachinjirizidwa ndi Zimene Anaŵerenga, 9/8
Kukongola kwa Mkati (Geode), 2/8
“Mfungulo ku Ngozi” (Mfuti), 6/8
Miyambo ya Krisimasi, 12/8
Zimene Mwana Wosabadwa Amadziŵa, 11/8
NYAMA NDI ZOMERA
“Imodzi ya Ntchito Zaluso Zachibadwa” (Njovu), 3/8
SAYANSI
“Chilengedwe cha Ponseponse Chonse Mkati mwa Chigaza,” 2/8
Yochepera koma Yokhala ndi Zitsogozo Zapadera (DNA), 8/8
UMOYO NDI MANKHWALA
Kodi Kutaya Kulemera Kuli Nkhondo Yosagonjetseka? 6/8
Kusuta, 7/8, 8/8
Mwazi: Chosankha Chandani ndi Chikumbumtima Chandani? 3/8
Njira Zinayi Zopambanira, 6/8
Nsabwe za M’mutu, 9/8
Thandizo kwa Okhala ndi Zosoŵa Zapadera (Kulemala Kwa Nzeru Zodziŵira Zinthu), 8/8
Umoyo Wabwino, 12/8
ZOCHITIKA ZADZIKO NDI MIKHALIDWE
Chipululutso, 4/8
Chiwawa—Kodi Tikuchifikira Chitokoso? 5/8
Chiwawa—Mapeto Akuwonekera, 5/8
Dziko Lopanda Zida, 6/8
Kodi Nchiyani Chikuchitika ku Makhalidwe? 8/8
Kodi Nchiyani Chimene Chikuchitika ku Maseŵera? 11/8
Kufunafuna Mtendere ndi Chisungiko, 12/8
Kuyendayenda mu Imfa (Zida Zankhondo), 6/8
Malonda a Zida Zankhondo, 6/8
Nkhondo—Kuchita ndi Zotulukapo Zake, 10/8