Tsamba 2
Kumwa ndi Kuyendetsa Galimoto 3-13
Padziko lonse, anthu 300,000 amaphedwa ndipo mamiliyoni ambirimbiri amavulazidwa chaka chirichonse m’ngozi zagalimoto, kusakaza kwambiri kumachititsidwa ndi oyendetsa galimoto omwe ankamwa. Kodi vutoli lidzakhoza kuthetsedwa?
Kodi Mumadana ndi Kulandira Chisulizo? 28
Anthu ambiri amatero. Muno muli njira zisanu ndi imodzi zokuthandizani kuchotsa, kapenatu kuchepetsa, kuwawa kwa kusuliza.