Tsamba 2
Pamene Munthu ndi Chilombo Akhala Pamtendere 3-11
Anthu ambiri amasangalala ndi nyama zam’mudzi monga ziweto. Koma bwanji ponena za zilombo zakuthengo? Kodi izo zidzakhalapo konse pamtendere weniweni ndi anthu, popanda kutsekeredwa m’zikwere?
Kuchinjiriza Kuberanso kwa Zizoloŵezi Zoipa 28
Kodi munalakapo zizoloŵezi zoipa ndiyeno mungowona kuti zabweranso ndikugwiraninso mwamphamvu? Kodi ndimotani mmene mungachinjirizire zimenezi?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Chikuto, 2, 10: Fanizo la msungwana ali ndi ana a nyalugwe lozikidwa pa chilolezo cha Hartebeespoortdam Snake and Animal Park