Tsamba 2
Pearl Harbor ndi Hiroshima—Kodi Kusweka Mtimako Kudzathadi? 3-11
Zaka makumi asanu zapitazo kuukira Pearl Harbor kwa Japani kunayambitsa nkhondo mu Pacific. Nkhondoyo inatha ndi kuphulitsidwa kwa bomba la atomu pa Hiroshima ndi Nagasaki. Kwa anthu ambiri, kukumbukira nkhondoyo kumadzutsa kusweka mtima kwakale. Kodi kusweka mtimako kudzathadi?
Chifukwa Chake Krisimasi Siiri ya Akristu 12
Kodi Krisimasi inachokera kuti? Chifukwa chake Yesu sanaivomereze.
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Cover Picture: Left, USAF photo. Right, U.S. Navy photo.