Zisonyezero za Volyumu 35 ya Galamukani!
ACHICHEPERE AKUFUNSA KUTI
Bwanji Nanga za Zinthu Zapamtima? 12/8
Kodi Bwanji Ponena za Makalabu Ausiku? 2/8
Kodi Kugwiritsira Ntchito Mawu Onyodola Kuli ndi Chivulazo Chotani? 10/8
Kodi Kusuta Kulidi Koipa Motero? 8/8
Kodi Kutchova Njuga Kuli Koipa Motero? 11/8
Kodi Kutyasira Kuli Nchivulazo Chotani? 5/8
Kodi Misonkhano Yachikristu Ingandithandize Motani? 7/8
Kodi Nchifukwa Ninji Makolo Anga Amayesayesa Kulamulira Moyo Wanga? 5/8
Kodi Nchifukwa Ninji Sindimayenererana Nawo? 11/8
“Kodi Nchifukwa Ninji Sindingamalize Zimene Ndayamba?” 9/8
Kodi Ndiloŵe m’Timu Yasukulu? 7/8
Kodi Ndimotani Mmene Ndingakhalire Chitsanzo kwa Ang’ono Anga? 4/8
Kodi Ndingachikanize Motani Chitsenderezo cha Kusuta? 9/8
Kodi Ndingadzichinjirize Motani ku Kuukiridwa ndi Gulu? 8/8
Kodi Ndingakhale Bwanji Wachimwemwe ndi Kholo Limodzi Lokha? 1/8
Kodi Ndingakhale Bwanji Mlezi Wabwino wa Ana? 3/8
Kodi Ndingakhale Motani M’banja Logaŵikana Mwachipembedzo? 2/8
Kodi Ndingampangitse Motani Kuleka Kundivuta? 6/8, 10/8
Kodi Ndingapeŵe Motani Kupweteka kwa Kutyasira? 12/8
Kodi Ndingathandize Motani Kholo Langa Limodzi? 4/8
Kodi Ndiyenera Kugwira Ntchito Pamene Ndidakali Pasukulu? 1/8
Kodi Ndiyenera Kukhaliranji Mlezi wa Ana? 3/8
Kodi Ndiyenera Kuphatikana ndi Gulu? 6/8
CHIPEMBEDZO
Baibulo Linalimbana ndi Matenda Sayansi Isanatero, 12/8
Bungwe la Matchalitchi Lapadziko Lonse, 11/8
Kodi Iwo Amamamatira ku Zonena Zawo? 1/8
Kugwirizanitsa Matchalitchi? 3/8
Kum’mawa kwa Yuropu—Kodi Kukuvomerezanso Chipembedzo? 1/8
Kupanikizika kwa Tchalitchi cha Katolika, 3/8
Zoyesayesa za Kugwirizanitsa 3/8
CHUMA NDI NTCHITO YOLEMBEDWA
Chothetsa Nzeru cha Wolembedwa Ntchito, 8/8
Mutachotsedwa Ntchito, 8/8
LINGALIRO LABAIBULO
Imfa ya Mwana, 3/8
Kodi Nkuphunziriranji Baibulo? 10/8
Krisimasi Siiri ya Akristu, 12/8
Kudzichinjiriza, 7/8
Kugwira Njoka, 4/8
Kutsimikizira—Kodi Kuli Chiyeneretso Chachikristu? 8/8
Masiku Akulenga, 6/8
Mitala, 5/8
Zakumwa Zoledzeretsa, 11/8
Zaumaliseche, 9/8
MAIKO NDI ANTHU
Kukulira Mumzinda wa mu Afirika, 11/8
Luso Lapadera la Madagascar, 9/8
Pont du Gard, 12/8
Saudi Arabia, 1/8
Tsiku Limodzi m’Moyo Wanga (Hong Kong), 11/8
MAUNANSI A ANTHU
Chithandizo kwa Ana a m’Chisudzulo, 5/8
Chithandizo kwa Omafa, 11/8
Kodi Mumadana ndi Kulandira Chisulizo? 2/8
Kuchezera Odwala, 3/8
Kuchitira Nkhanza Ana, 10/8
Kukondana Mwakungowonana Koyamba, 10/8
Kulankhulana kwa Dokotala ndi Wodwala, 3/8
Kulemekeza Okalamba, 4/8
Kulera Mabanja Padziko Lonse, 10/8
Mabala Obisika, 10/8
Mabanja—Gwirizanani, 10/8
Minkhole ya Kuchitira Nkhanza Ana, 10/8
Miseche—Peŵani Kuvulazidwa, 6/8
MBONI ZA YEHOVA
Chikhulupiriro Chisuntha Mapiri (Argentina), 7/8
Kodi Ndiuthenga Uti Womwe Akuwumva? 1/8
Kulaka Moyo Wachiwawa, 8/8
Kum’mawa kwa Yuropu, 1/8
Kupititsa Patsogolo Maopareshoni Opanda Mwazi, 12/8
Kutamanda Yehova m’Kuimba (South Africa), 12/8
Makalata a Chiyamikiro, 6/8, 7/8
Mphamvu Yosintha ya Chowonadi (R. Pryor), 8/8
Soviet Union, 1/8
NKHANI ZOSIYANASIYANA
Kodi Kukhala Wowona Mtima Kumapereka Mphotho? 11/8
Kodi Nkusinthiranji? 7/8
Kusintha Amene Muli? 7/8
Malo Omwe Maseŵera Ali Nawo, 9/8
Mliri wa Lotale, 5/8
“Simlandu Wanga!” 3/8
Zikumbukiro—Mwakungosinika Batani! 7/8
Zizoloŵezi Zoipa, 4/8
NYAMA NDI ZOMERA
Bwanji Ponena za Mtsogolo? 4/8
Chimbalangondo Choyera cha Kumalo Ozizira, 6/8
Kodi Munthu ndi Chilombo Angakhale Pamtendere? 4/8
Kuganiza kwa Nyani, 10/8
Pamene Munthu ndi Chilombo Akhala Pamtendere, 4/8
Zopinga Mtendere, 4/8
ULAMULIRO WA ANTHU UYESEDWA
Pomalizira Papezeka Boma Langwiro, 1/8
UMOYO NDI MANKHWALA
AIDS—Imfa Yake Yowopsa pa Ana, 8/8
AIDS ndi Lingaliro Lachinyengo la Chisungiko, 3/8
AIDS—Vuto la Azaka Zapakati pa 13 ndi 19, 8/8
AIDS—Zimene Makolo ndi Ana Ayenera Kudziŵa, 8/8
Baibulo Linayamba Kulimbana ndi Matenda Sayansi Isanatero, 12/8
Chithandizo kwa Odwala Mosachiritsika, 11/8
Chithandizo kwa Omafa, 12/8
Kuchitira Nkhanza Ana, 10/8
Kupititsa Patsogolo Maopareshoni Opanda Mwazi, 12/8
Mmene Adokotala Amapeŵera AIDS, 7/8
Nanga Nkuchitiranji? (Kusuta), 5/8
“Osafooka,” 9/8
Vuto la Khofi, 5/8
Wochokera m’Zigama (TMJ Syndrome), 7/8
Zipatala, 3/8
ZOCHITIKA ZA DZIKO NDI MAKHALIDWE
“Anthu Okhala Ngati Mfuko” (Kusoŵa pokhala), 4/8
Chifukwa Chake Chigwirizano Chinafunikira, 9/8
Dziko Losadziletsa, 2/8
Dziko Lotchova Njuga, 2/8
Kodi Fodya Ngwabwino? 2/8
Kumwa ndi Kuyendetsa Galimoto, 2/8
Kuwonjezereka Kwakukulu kwa Anthu, 11/8
Minkhole Iyang’anizana ndi Aliŵongo, 2/8
Mitundu Yogwirizana, 9/8
Mliri wa Lotale, 5/8
Mpira Wachitanyu Wolimbirana Chikho Chapadziko Lonse, 5/8
Msanganizo Wakupha, 2/8
“Ndikuchifuna Tsopanoli!” 2/8
‘Ndipo Khoma Linagwa Pansi,’ 1/8
Nkhalango Zomazimiririka, Kutentha Komawonjezereka, 2/8
Pearl Harbor ndi Hiroshima, 12/8
“Sitifunanso Mahiroshima Ena!” 12/8
Wailesi Yakanema, 6/8