Tsamba 2
Chisudzulo—Zimene Anthu Amataikiridwa 3-10
Okwatirana mamiliyoni ambiri amasudzulana chaka chirichonse. Mbadwo wathu wawona kuwonjezereka kodabwitsa kwa zisudzulo padziko lonse. Kodi nchiyani chimene chimanyenga anthu kuti asudzulane, ndipo kodi amataikiridwanji?
Malonda Aumbombo Asonyeza Mkhalidwe Wake Weniweni 29
Kodi ndimotani mmene malonda anayambira m’zaka za zana la 15 kumkabe mtsogolo? Kodi ukapolo unachita mbali yotani? Kodi zolinga zenizeni za malonda nzotani?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Harper’s Encyclopædia of United States History