Tsamba 2
Kugwiriridwa Chigololo Nkhaŵa ya Mkazi 3-11
Kodi nchiyani chimasonkhezera wogwirira chigololo? Kodi akazi angachitenji kuti apewe kugwiriridwa chigololo? Kodi nchiyani chimene chidzaletsa amuna kukhala ogwirira chigololo? Mafunso ameneŵa ndi ena adzayankhidwa m’mpambo wotsekulira.
Kodi Ndiyenera Kupita ku Prom? 17
M’maiko ena, kumaliza maphunziro a sukulu yasekondale kumaphatikizapo kuchita phwando ndi kuvina. Kaŵirikaŵiri kumatsogolera kukhalidwe loipa ndi zoipirapo. Kodi ndimotani mmene Mkristu wosamala ayenera kulingalilira prom?