Tsamba 2
Olakika Poyang’anizana ndi Imfa 3-12
Udani wautundu ndi ndale, wamafuko, ndi wachipembedzo wachititsa nkhondo, ndewu, ndi chizunzo. Pakhala mikhole mamiliyoni ambiri ndi ophedwera chikhulupiriro zikwi zambiri. Kodi kusiyana nkotani? Kodi chilakiko chikhalapo bwanji?
Chipembedzo ndi Sayansi—Msanganizo Woipa 17
Maphunziro achipembedzo, alchemy, ndi sayansi zinali zogwirizana m’zaka mazana ambiri zapita. Kodi chinatsatirapo nchiyani?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Musei Capitolini, Roma