Tsamba 2
Nyimbo Zamakono Kodi Nzosangulutsa Zosavulaza? 3-11
Nyimbo zamakono, monga ngati za heavy metal ndi rap, zayamba kusulizidwa. Kodi nyimbo zonse zoterozo nzoipa, kapena kodi zina nzosangulutsa zosavulaza?
Kodi Ndingalake Motani Kupunduka Kwanga? 16
Achichepere opunduka amafuna kudziŵa mmene angachitire ndi mkhalidwewo.
Zopereka Zothandizira Osauka—Kodi Ndithayo Lachikristu? 22
Kodi kawonedwe kachikatikati kakupereka chopereka ku magulu achipembedzo kapena magulu ena nkotani?