Tsamba 2
Kodi Makhalidwe Akumka Kuti? 3-10
M’mbali zonse za moyo—chipembedzo, chuma, ndale, kakhalidwe ka anthu, zakugonana—makhalidwe akusintha. Kodi nchifukwa ninji zili choncho? Kodi zonsezi zikumka kuti?
Kodi “Chipangano Chatsopano” Chimatsutsa Ayuda? 11
Ena amanena kuti “Chipangano Chatsopano” chimatsutsa Ayuda. Kodi zimenezi nzowona?