Tsamba 2
Achichepere Amene Amaika Mulungu Poyamba 3-15
M’nthaŵi zakale zikwi za achichepere zinafa chifukwa cha kuika Mulungu poyamba. Iwo akuchitabe zimenezo, kokha kuti lerolino zinthuzo zikuchitikira m’zipatala ndi m’mabwalo amilandu, pa nkhani ya kuthiridwa mwazi.
Bwanji Ngati Ndikondana ndi Wosakhulupirira? 26
Mungasweke mtima ngati munyalanyaza uphungu wa ‘kukwatira [kokha, NW] mwa Ambuye.’