Tsamba 2
Kodi Muyenera Kutsogoza Moyo Wanu ndi Nyenyezi? 3-8
Mamiliyoni a anthu amapenda horoscope tsiku ndi tsiku. Kodi nyenyezi zingayambukiredi miyoyo yathu? Kodi nyenyezi zili ndi ntchito yotani m’Baibulo? Kodi zingatiphunzitsenji?
Maseŵera Ochititsa Nthumanzi—Kodi Ndiyenera Kuwayesa? 9
Zochitika zamaseŵera zambiri zimaloŵetsamo ngozi—zina zimaposa zinzake. Kodi ndimotani mmene Mkristu ayenera kuonera kutenga nawo mbali m’maseŵera otero?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Cover: Courtesy of ROE/Anglo-Australian Observatory, photograph by David Malin