Tsamba 2
MAKOLO Khalani Ochirikiza! 3-10
Mavuto m’madongosolo a sukulu awonjezereka kwambiri m’zaka zaposachedwapa. Kodi makolo angathandize motani ana awo kulimbana nawo?
Kodi Kutchova Juga ndi kwa Akristu? 20
Kutchova juga, kololedwa mwalamulo kapena kosaloledwa, kuli kofalikira. Kodi lingaliro Lachikristu nlotani?
Kodi Ndingachotse Motani Maganizo Anga pa Osiyana Nawo Ziŵalo? 25
Achichepere akufuna kudziŵa zimene angachite kuti alamulire maganizo awo pankhani imeneyi.
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Valentin/The Cheaters, Giraudon/Art Resource