Tsamba 2
1914 Kuwomberedwa Mfuti Kumene Kukali Kugwedeza Dziko Lathu 3-11
Kuphedwa mwa chiwembu kwa Archduke Ferdinand wa ku Austria ndi mkazi wake kunayambitsa Nkhondo Yadziko I. Kodi ndimotani mmene nkhani zimene zinakhudza maiko a Balkan panthaŵiyo zikali kugwedezera dziko lathu lerolino?
Kodi Ndachita Tchimo Losakhululukidwa? 18
Achichepere ambiri oona mtima, ndi achikulire omwe, amayambukiridwa kwambiri ndi machimo ndi zifooko zawo. Koma kodi machimo ameneŵa alidi osakhululukidwa?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
The Bettmann Archive
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Chithunzi pachikuto: Kuwomberedwa mfuti kwa Archduke Ferdinand kojambulidwa ndi katswiri: Culver Pictures