Tsamba 2
Kodi Ano Ndiwo Masiku Otsiriza? 3-11
Popeza kuti Baibulo lili ngati mapu a msewu, kodi ilo limasonyeza pamene tili? Kodi tikukhala m’masiku otsiriza? Ngati ndi choncho, kodi nchiyani chimene chili patsogolopa? Kodi tiyenera kuchitanji?
Zaka Zoposa 40 Pansi pa Chiletso cha Komyunizimu 19
Mboni za Yehova zambiri ku Eastern Europe zinakhala ndi moyo pansi pa chiletso kwa zaka zoposa 40. Ŵerengani zokumana nazo zokondweretsa za Mboni ina Yachitcheki.
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
CHIKUTO: Kuzungulira kuyambira kulamanja kumka kulamanzere, Majeti ankhondo: Chithunzi cha USAF; Laŵi la moto: Tina Gerson/Los Angeles Daily News; Jeti yoponya mabomba: Mwachilolezo cha Unduna wa Zachitetezo, London; Msilikali: Chithunzi cha U.S. National Archives (onaninso masamba 2, 7); TSAMBA LACHIŴIRI: Kuphulika kwa bomba la nyukliya: Chithunzi cha U.S. National Archives (onaninso tsamba 7); Mwana wanjala: Mark Peters/Sipa Press (onaninso tsamba 8)